Numeri 17:12 - Buku Lopatulika12 Pamenepo ana a Israele ananena ndi Mose, nati, Taonani, tikufa, tionongeka, tionongeka tonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Pamenepo ana a Israele ananena ndi Mose, nati, Taonani, tikufa, tionongeka, tionongeka tonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tsono Aisraele adauza Mose kuti, “Tatayika, tonsefe taferatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Aisraeli anati kwa Mose, “Tikufa! Tatayika, tonse tatayika! Onani mutuwo |