Numeri 17:13 - Buku Lopatulika13 Yense wakuyandikiza chihema cha Yehova amwalira; kodi tidzatha nkufa? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Yense wakuyandikiza Kachisi wa Yehova amwalira; kodi tidzatha nkufa? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Ngati munthu aliyense amene akuyandikira chihema cha Chauta alikufa, ndiye kuti tonsefe ndife akufa.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Aliyense woyandikira chihema adzafa. Kodi ndiye kuti tonse tikufa?” Onani mutuwo |