Numeri 15:6 - Buku Lopatulika6 Kapena ukonzere nkhosa yamphongo nsembe yaufa, awiri mwa magawo khumi a efa wa ufa wosalala, wosakaniza ndi mafuta, limodzi la magawo atatu la hini. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Kapena ukonzere nkhosa yamphongo nsembe yaufa, awiri mwa magawo khumi a efa wa ufa wosalala, wosanganiza ndi mafuta, limodzi la magawo atatu la hini. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ikakhala nkhosa yamphongo, muzipereka chopereka cha chakudya cholemera makilogaramu aŵiri, wosakaniza ndi mafuta okwanira lita limodzi ndi theka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 “Pamodzi ndi nkhosa yayimuna, muzikakonzanso chopereka cha chakudya cholemera makilogalamu awiri a ufa wosalala, wosakaniza ndi mafuta okwanira lita imodzi ndi theka, Onani mutuwo |