Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 15:6 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 “Pamodzi ndi nkhosa yayimuna, muzikakonzanso chopereka cha chakudya cholemera makilogalamu awiri a ufa wosalala, wosakaniza ndi mafuta okwanira lita imodzi ndi theka,

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

6 Kapena ukonzere nkhosa yamphongo nsembe yaufa, awiri mwa magawo khumi a efa wa ufa wosalala, wosakaniza ndi mafuta, limodzi la magawo atatu la hini.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 Kapena ukonzere nkhosa yamphongo nsembe yaufa, awiri mwa magawo khumi a efa wa ufa wosalala, wosanganiza ndi mafuta, limodzi la magawo atatu la hini.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Ikakhala nkhosa yamphongo, muzipereka chopereka cha chakudya cholemera makilogaramu aŵiri, wosakaniza ndi mafuta okwanira lita limodzi ndi theka.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 15:6
5 Mawu Ofanana  

“ ‘Ngati munthuyo apereka mbuzi ngati nsembe, abwere nayo kwa Yehova.


munthu amene akubweretsa zopereka zake, azikapereka kwa Yehova chopereka chachakudya cholemera kilogalamu imodzi ya ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta wokwana lita imodzi.


Pamodzi ndi mwana wankhosa aliyense wa nsembe yopsereza kapena nsembe ina, muzikakonzanso lita imodzi la vinyo ngati chopereka cha chakumwa.’ ”


ndi vinyo wokwanira lita imodzi ndi theka ngati chopereka cha chakumwa. Muzikapereka monga nsembe yopereka fungo lokoma kwa Yehova.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa