Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Numeri 11:6 - Buku Lopatulika

6 koma tsopano moyo wathu waphwa; tilibe kanthu pamaso pathu koma mana awa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

6 koma tsopano moyo wathu waphwa; tilibe kanthu pamaso pathu koma mana awa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

6 Koma tsopano mphamvu zathu zatha, ndipo sitikuwona kanthu kena kakudya koma mana basi.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

6 Koma tsopano chilakolako chathu chatha. Sitikuona kanthu kena kakudya koma mana basi!”

Onani mutuwo Koperani




Numeri 11:6
3 Mawu Ofanana  

Nanena naye, Iwe mwana wa mfumu, uonderanji tsiku ndi tsiku? Sungandiuze kodi? Ndipo Aminoni anati kwa iye, Ndikonda Tamara, mlongo wa mbale wanga Abisalomu.


Koma chilekere ife kufukizira mfumu yaikazi ya kumwamba, ndi kumthirira iye nsembe zothira, tasowa zonse, tathedwa ndi lupanga ndi njala.


Ndipo anthu ananena motsutsana ndi Mulungu, ndi Mose, ndi kuti, Mwatikwezeranji kutichotsa ku Ejipito kuti tifere m'chipululu? Pakuti mkate ndi madzi palibe, ndi mtima wathu walema nao mkate wachabe uwu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa