Numeri 11:5 - Buku Lopatulika5 Tikumbukira nsomba tinazidya mu Ejipito chabe, minkhaka, ndi mavwende, ndi anyezi wa mitundu itatu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Tikumbukira nsomba tinazidya m'Ejipito chabe, minkhaka, ndi mavwende, ndi anyezi a mitundu itatu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tikukumbukira nsomba zaulere zimene tinkadya ku Ejipito, minkhaka ija, mavwende ndi anyezi wamitundu-mitundu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Tikukumbukira nsomba zaulere zimene tinkadya ku Igupto komanso nkhaka, mavwende, anyezi wamitundumitundu ndi adyo. Onani mutuwo |