Numeri 11:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo mana ananga zipatso zampasa, ndi maonekedwe ake ngati maonekedwe a bedola. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo mana ananga zipatso zampasa, ndi maonekedwe ake ngati maonekedwe a bedola. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Manayo ankafanafana ndi njere za mapira, ndipo maonekedwe ake anali ngati ulimbo wouma. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mana ankafanana ndi mbewu zamapira ndipo maonekedwe ake anali ngati ulimbo wowuma. Onani mutuwo |