Numeri 1:52 - Buku Lopatulika52 Ndipo ana a Israele amange mahema ao, yense ku chigono chake, ndi yense ku mbendera yake, monga mwa makamu ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201452 Ndipo ana a Israele amange mahema ao, yense ku chigono chake, ndi yense ku mbendera yake, monga mwa makamu ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa52 Aisraele azimanga mahema ao m'magulumagulu, aliyense pa chithando chake, ndipo onse azimanga pafupi ndi mbendera yao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero52 Aisraeli azimanga matenti awo mʼmagulumagulu, munthu aliyense ku gulu lake pansi pa mbendera yake. Onani mutuwo |