Numeri 1:51 - Buku Lopatulika51 Ndipo akati amuke nacho chihemacho, Alevi amgwetse, ndipo akati achimange, Alevi achiimike; ndipo mlendo akayandikizako amuphe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201451 Ndipo akati amuke naye Kachisiyo, Alevi amgwetse, ndipo akati ammange, Alevi amuimike; ndipo mlendo akayandikizako amuphe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa51 Nthaŵi imene anthu akunyamuka ulendo, Alevi ndiwo amene azichitsitsa, ndipo nthaŵi imene anthu aima, Alevi omwewo ndiwo amene azichiimiritsa. Munthu wina aliyense wochiyandikira adzaphedwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero51 Pamene akusamutsa tentiyo, Alevi ndiwo aziyitsitsa, akafuna kuyimanganso, Alevi ndiwo aziyimiritsa. Wina aliyense amene adzayandikire tentiyo adzaphedwa. Onani mutuwo |