Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Numeri 1:52 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

52 Aisraeli azimanga matenti awo mʼmagulumagulu, munthu aliyense ku gulu lake pansi pa mbendera yake.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

52 Ndipo ana a Israele amange mahema ao, yense ku chigono chake, ndi yense ku mbendera yake, monga mwa makamu ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

52 Ndipo ana a Israele amange mahema ao, yense ku chigono chake, ndi yense ku mbendera yake, monga mwa makamu ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

52 Aisraele azimanga mahema ao m'magulumagulu, aliyense pa chithando chake, ndipo onse azimanga pafupi ndi mbendera yao.

Onani mutuwo Koperani




Numeri 1:52
4 Mawu Ofanana  

“Aisraeli azimanga misasa yawo mozungulira tenti ya msonkhano motalikira pangʼono. Munthu aliyense amange pamene pali mbendera ya fuko lake.”


Choncho Aisraeli anachita zonse zomwe Yehova analamulira Mose. Umo ndi momwe amamangira misasa yawo pamene panali mbendera zawo, ndipo ankasamuka monga mwa mafuko a makolo awo.


Balaamu atayangʼana, anaona Aisraeli atamanga misasa yawo fuko ndi fuko. Pamenepo mzimu wa Mulungu unabwera pa iye


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa