Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 6:8 - Buku Lopatulika

8 Pakuti wanzeru ali ndi chiyani choposa chitsiru? Waumphawi wodziwa kuyenda pamaso pa amoyo ali ndi chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Pakuti wanzeru ali ndi chiyani choposa chitsiru? Waumphawi wodziwa kuyenda pamaso pa amoyo ali ndi chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Nanga munthu wanzeru ali ndi chiyani chimene amapambana nacho chitsiru? Kodi mmphaŵi amene amangodziŵa kukhala bwino pamaso pa anzake, ndiye kuti wapindulapo chiyani?

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Kodi munthu wanzeru amaposa motani chitsiru? Kodi munthu wosauka amapindula chiyani podziwa kukhala bwino pamaso pa anthu ena?

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 6:8
9 Mawu Ofanana  

Pamene Abramu anali wa zaka makumi asanu ndi anai kudza zisanu ndi zinai, Yehova anamuonekera Abramu nati kwa iye, Ine ndine Mulungu Wamphamvuyonse; yenda iwe pamaso panga, nukhale wangwiro.


Ndidzachita mwanzeru m'njira yangwiro; mudzandidzera liti? Ndidzayenda m'nyumba mwanu ndi mtima wangwiro.


Ndidzayenda pamaso pa Yehova m'dziko la amoyo.


Wosauka woyenda mwangwiro aposa wokhetsa milomo ndi wopusa.


Pochuluka katundu, akudyapo achulukanso; nanga apindulira eni ake chiyani, koma kungopenyera ndi maso ao?


Kupenya kwa maso kuposa kukhumba kwa mtima; ichinso ndi chabe ndi kungosautsa mtima.


Ndipo onse awiri anali olungama mtima pamaso pa Mulungu, namayendabe m'malamulo onse ndi zoikika za Ambuye osachimwa.


Lamulira iwo achuma m'nthawi ino ya pansi pano, kuti asadzikuze, kapena asayembekezere chuma chosadziwika kukhala kwake, koma Mulungu, amene atipatsa ife zonse kochulukira, kuti tikondwere nazo;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa