Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 6:7 - Buku Lopatulika

7 Ntchito zake zonse munthu angogwirira m'kamwa mwake, koma mtima wake sukhuta.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ntchito zake zonse munthu angogwirira m'kamwa mwake, koma mtima wake sukhuta.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Munthu amagwira ntchito zolemetsa kuti apeze chakudya, komabe satha kukhutira kotheratu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ntchito yonse ya munthu imathera pakamwa pake, komatu iye sakhutitsidwa ndi pangʼono pomwe.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 6:7
11 Mawu Ofanana  

Wantchito adzigwirira yekha ntchito; pakuti m'kamwa mwake mumfulumiza.


Zinthu zonse zilemetsa; munthu sangathe kuzifotokoza; maso sakhuta m'kuona, ndi makutu sakhuta m'kumva.


Wokonda siliva sadzakhuta siliva; ngakhale wokonda chuma sadzakhuta phindu; ichinso ndi chabe.


Phindutu la dziko lipindulira onse; ngakhale mfumu munda umthandiza;


Chinkana munthu akabala ana makumi khumi, nakhala ndi moyo zaka zambiri, masiku a zaka zake ndi kuchuluka, koma mtima wake osakhuta zabwino, ndiponso alibe maliro; nditi, Nsenye iposa ameneyo;


Pakuti wanzeru ali ndi chiyani choposa chitsiru? Waumphawi wodziwa kuyenda pamaso pa amoyo ali ndi chiyani?


Chifukwa chake ndinena kwa inu, Musadere nkhawa moyo wanu, chimene mudzadya ndi chimene mudzamwa; kapena thupi lanu, chimene mudzavala. Kodi moyo suli woposa chakudya, ndi thupi loposa chovala?


Ndipo ndidzati kwa moyo wanga, Moyo iwe, uli nacho chuma chambiri chosungika kufikira zaka zambiri; tapumulatu, nudye, numwe, nukondwere.


Gwirani ntchito si chifukwa cha chakudya chimene chitayika koma cha chakudya chimene chitsalira kumoyo wosatha, chimene Mwana wa Munthu adzakupatsani inu; pakuti ameneyo Atate, ndiye Mulungu, adamlembera chizindikiro.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa