Mlaliki 6:4 - Buku Lopatulika4 pakuti ikudza mwachabe, nichoka mumdima, mdima nukwirira dzina lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 pakuti ikudza mwachabe, nichoka mumdima, mdima nukwirira dzina lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mtayo umangopita pachabe nkuloŵa mu mdima, ndipo umakaiŵalika mumdimamo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mtayo umangopita pachabe ndipo umapita mu mdima, ndipo mu mdimamo dzina lake limayiwalika. Onani mutuwo |