Mlaliki 6:5 - Buku Lopatulika5 Ngakhale dzuwa siliona ngakhale kulidziwa, imeneyi ipambana winayo kupuma; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ngakhale dzuwa siliona ngakhale kulidziwa, imeneyi ipambana winayo kupuma; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ngakhale mtayowo sudaone dzuŵa kapena kudziŵa kanthu kalikonse, komabe umapumula kupambana munthu wa moyo wautali uja, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ngakhale kuti mtayowo sunaone dzuwa kapena kudziwa kanthu kalikonse, koma umapumula kuposa munthu uja, Onani mutuwo |