Mlaliki 6:1 - Buku Lopatulika1 Pali choipa ndachiona kunja kuno chifalikira mwa anthu, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pali choipa ndachiona kunja kuno chifalikira mwa anthu, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Choipa china chimene ndachiwona pansi pano, chimene chimaŵaŵa anthu zedi, ndi ichi: Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ine ndinaona choyipa china pansi pano, ndipo chimasautsa anthu kwambiri: Onani mutuwo |