Mlaliki 5:20 - Buku Lopatulika20 Pakuti sadzakumbukira masiku a moyo wake kwambiri; chifukwa Mulungu amvomereza m'chimwemwe cha mtima wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Pakuti sadzakumbukira masiku a moyo wake kwambiri; chifukwa Mulungu amvomereza m'chimwemwe cha mtima wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Munthu wotereyu sadzaganizako kwenikweni za kuchepa kwa masiku a moyo wake, chifukwa chakuti Mulungu wamdzaza ndi chimwemwe mu mtima. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Munthu wotereyu saganizirapo za masiku a moyo wake, chifukwa Mulungu amamutanganidwitsa ndi chisangalalo cha mu mtima mwake. Onani mutuwo |