Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 11:4 - Buku Lopatulika

4 Woyang'ana mphepo sadzafesa; ndi wopenya mitambo sadzakolola.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Woyang'ana mphepo sadzafesa; ndi wopenya mitambo sadzakolola.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Amene ayembekeza kuti mphepo ikhale bwino, kapena kuti mitambo ibwere bwino, sadzabzala ndipo sadzakolola kanthu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Amene amayangʼana mphepo sadzadzala; amene amayangʼana mitambo sadzakolola.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 11:4
5 Mawu Ofanana  

Waulesi salima chifukwa cha chisanu; adzapemphapempha m'masika osalandira kanthu.


Waulesi ati, Pali mkango panjapo, ndidzaphedwa pamakwalalapo.


Oyenera kulandira zabwino usawamane; pokhoza dzanja lako kuwachitira zabwino.


Mitambo ikadzala mvula, itsanulira pansi; mtengo ukagwa kumwera pena kumpoto, pomwe unagwa mtengowo udzakhala pomwepo.


Monga sudziwa njira ya mphepo, ngakhale makulidwe a mafupa m'mimba ya mkazi ali ndi pakati; momwemo sudziwa ntchito za Mulungu amene achita zonse.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa