Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 11:3 - Buku Lopatulika

3 Mitambo ikadzala mvula, itsanulira pansi; mtengo ukagwa kumwera pena kumpoto, pomwe unagwa mtengowo udzakhala pomwepo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mitambo ikadzala mvula, itsanulira pansi; mtengo ukagwa kumwera pena kumpoto, pomwe unagwa mtengowo udzakhala pomwepo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Mitambo ikadzaza ndi madzi, kumagwa mvula. Mtengo ukagwera chakumwera kapena chakumpoto, kumene wagwerako kogonera nkomweko.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Ngati mitambo yadzaza ndi madzi, imagwetsa mvula pa dziko lapansi. Mtengo ukagwera cha kummwera kapena cha kumpoto, ndiye kuti udzagonera kumene wagwerako.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 11:3
9 Mawu Ofanana  

Ndipo kunali, polinda kanthawi, thambo linada ndi mitambo ndi mphepo, nigwa mvula yaikulu. Ndipo Ahabu anayenda m'galeta, namuka ku Yezireele.


Gawira asanu ndi awiri ngakhale asanu ndi atatu; pakuti sudziwa choipa chanji chidzaoneka pansi pano.


Woyang'ana mphepo sadzafesa; ndi wopenya mitambo sadzakolola.


Ndiponso tsopano lino nkhwangwa yaikidwa pa mizu ya mitengo: chifukwa chake mtengo uliwonse wosabala zipatso zabwino udulidwa nuponyedwa pamoto.


Ndipo anati kwa wosungira munda wampesa, Taona, zaka zapita zitatu ndimadza ine kudzafuna chipatso pa mkuyu uwu, ndipo ndimapeza palibe: taulikha; uyeseranjinso nthaka yopanda pake?


Koma iye amene ali nacho chuma cha dziko lapansi, naona mbale wake ali wosowa ndi kutsekereza chifundo chake pommana iye, nanga chikondi cha Mulungu chikhala mwa iye bwanji?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa