Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Mlaliki 1:11 - Buku Lopatulika

11 Zoyamba zija sizikumbukiridwa; ngakhale zomwe zilinkudzazo, omwe adzakhalabe m'tsogolomo, sadzazikumbukirai.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

11 Zoyamba zija sizikumbukiridwa; ngakhale zomwe zilinkudzazo, omwe adzakhalabe m'tsogolomo, sadzazikumbukirai.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

11 Zakale sizikumbukika, ngakhale zinthu zimene zidzachitike pambuyo pake sizidzakumbukikanso ndi amene adzabwere m'tsogolo mwake.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

11 Anthu akale sakumbukiridwa, ngakhale amene adzabwera mʼtsogolomu sadzakumbukiridwa ndi iwo amene adzabwere pambuyo pawo.

Onani mutuwo Koperani




Mlaliki 1:11
7 Mawu Ofanana  

Adaniwo atha psiti, apululuka nthawi zonse; ndipo mizindayo mwaipasula, chikumbukiro chao pamodzi chatha.


Kodi pali kanthu unganene kuti, Taona katsopano aka? Kanalipo kale, kale lomwe tisanabadwe ife.


Pakuti wanzeru saposa chitsiru kukumbukidwa nthawi zonse; pakuti zonse zooneka kale zidzaiwalika m'tsogolomo. Ndipo wanzeru amwalira bwanji ngati chitsirutu.


Ndipo ndinaona oipa alikuikidwa m'manda ndi kupita; ndipo omwe anachita zolungama anachokera kumalo opatulika akumzinda nawaiwala; ichinso ndi chabe.


Pakuti amoyo adziwa kuti tidzafa; koma akufa sadziwa kanthu bii, sadzalandira mphotho; pakuti angoiwalika.


Taona, zinthu zakale zaoneka, ndipo zatsopano Ine ndizitchula; zisanabuke ndidzakumvetsani.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa