Mlaliki 1:12 - Buku Lopatulika12 Ine Mlaliki ndinali mfumu ya Israele mu Yerusalemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ine Mlaliki ndinali mfumu ya Israele m'Yerusalemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ine Mlalikine ndidakhalapo mfumu yolamulira Israele ku Yerusalemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ine, Mlalikine, ndinali mfumu ya Israeli mu Yerusalemu. Onani mutuwo |