Mika 2:9 - Buku Lopatulika9 Muwataya akazi a anthu anga kunja kwa nyumba zao zokondweretsa; muchotsa ulemerero wanga kwa ana ao kosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Muwataya akazi a anthu anga kunja kwa nyumba zao zokondweretsa; muchotsa ulemerero wanga kwa ana ao kosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Akazi a anthu anga mumaŵatulutsa m'nyumba zao zokoma. Ndipo ana ao mumaŵalanda madalitso anga kosalekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mumatulutsa akazi a anthu anga mʼnyumba zawo zabwino. Mumalanda ana awo madalitso anga kosatha. Onani mutuwo |
Chifukwa chake mbuye wanga mfumu amvere mau a kapolo wake. Ngati ndi Yehova anakuutsirani inu kutsutsana ndi ine, alandire chopereka; koma ngati ndi ana a anthu, atembereredwe pamaso pa Yehova, pakuti anandipirikitsa lero kuti ndisalandireko cholowa cha Yehova, ndi kuti, Muka, utumikire milungu ina.