Mika 2:8 - Buku Lopatulika8 Koma ngakhale dzulo anthu anga anauka ngati mdani; mukwatula chofunda kumalaya a iwo opitirira mosatekeseka, ngati anthu osafuna nkhondo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Koma ngakhale dzulo anthu anga anauka ngati mdani; mukwatula chofunda kumalaya a iwo opitirira mosatekeseka, ngati anthu osafuna nkhondo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Chauta akuti, “Koma inu mumaukira anthu anga ngati mdani. Mumaŵavula mkanjo anthu amtendere, amene amangoyenda ndi mtima wokhazikika, osaganizako za nkhondo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Posachedwapa anthu anga andiwukira ngati mdani. Mumawavula mkanjo wamtengowapatali anthu amene amadutsa mosaopa kanthu, monga anthu amene akubwera ku nkhondo. Onani mutuwo |