Mika 2:10 - Buku Lopatulika10 Nyamukani, chokani, pakuti popumula panu si pano ai; chifukwa cha udyo wakuononga ndi chionongeko chachikulu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Nyamukani, chokani, pakuti popumula panu si pano ai; chifukwa cha udyo wakuononga ndi chionongeko chachikulu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Nyamukani, chokani, ano simalo opumulirapo. Zonyansa zanu zaŵaipitsa, zadzetsapo chiwonongeko choopsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Nyamukani, chokani! Pakuti ano si malo anu opumulirapo, chifukwa ayipitsidwa, awonongedwa, sangatheke kuwakonzanso. Onani mutuwo |