Mika 2:5 - Buku Lopatulika5 Chifukwa chake udzasowa woponya chingwe chamaere m'msonkhano wa Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Chifukwa chake udzasowa woponya chingwe chamaere m'msonkhano wa Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Tsono pa nthaŵi imene Chauta adzabwezeranso dziko kwa anthu ake, inuyo simudzalandirako gawo lililonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Nʼchifukwa chake simudzakhala ndi munthu mu msonkhano wa Yehova kuti agawe dziko pochita maere. Onani mutuwo |