Mika 2:6 - Buku Lopatulika6 Musamanenera, amanenera ati. Sadzanenera kwa awa; matonzo sadzachoka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Musamanenera, amanenera ati. Sadzanenera kwa awa; matonzo sadzachoka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Anthu amandiwuza kuti, “Musatilalikire, munthu asalalike zimenezi. Manyazi sadzatigwera ai. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Aneneri awo amanena kuti, “Usanenere! Usanenere ndi pangʼono pomwe zimenezi; ife sitidzachititsidwa manyazi.” Onani mutuwo |