Mateyu 26:3 - Buku Lopatulika3 Pomwepo anasonkhana ansembe aakulu, ndi akulu a anthu, kubwalo la mkulu wa ansembe, dzina lake Kayafa; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pomwepo anasonkhana ansembe aakulu, ndi akulu a anthu, kubwalo la mkulu wa ansembe, dzina lake Kayafa; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Nthaŵi imeneyo akulu a ansembe ndi akulu a Ayuda adasonkhana m'nyumba ya mkulu wa ansembe onse, dzina lake Kayafa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pamenepo akulu a ansembe ndi akuluakulu anasonkhana ku nyumba ya mkulu wa ansembe dzina lake Kayafa, Onani mutuwo |