Mateyu 1:3 - Buku Lopatulika3 ndi Yuda anabala Perezi ndi Zera mwa Tamara; ndi Perezi anabala Hezironi; ndi Hezironi anabala Ramu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndi Yuda anabala Perezi ndi Zera mwa Tamara; ndi Perezi anabala Hezironi; ndi Hezironi anabala Ramu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Yuda adabereka Perezi ndi Zera, mwa Tamara; Perezi adabereka Hezironi, Hezironi adabereka Ramu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Yuda anabereka Perezi ndi Zara, amene amayi awo anali Tamara. Perezi anabereka Hezironi, Hezironi anabereka Aramu. Onani mutuwo |