Masalimo 99:9 - Buku Lopatulika9 Mkwezeni Yehova Mulungu wathu, ndipo gwadirani paphiri lake loyera; pakuti Yehova Mulungu wathu ndiye woyera. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mkwezeni Yehova Mulungu wathu, ndipo gwadirani pa phiri lake loyera; pakuti Yehova Mulungu wathu ndiye woyera. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tamandani Chauta, Mulungu wathu, mpembedzeni ku phiri lake loyera. Chauta, Mulungu wathu, ndi woyera. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Kwezani Yehova Mulungu wathu ndipo mumulambire pa phiri lake loyera, pakuti Yehova Mulungu wathu ndi woyera. Onani mutuwo |