Masalimo 99:8 - Buku Lopatulika8 Munawayankha, Yehova Mulungu wathu: munawakhalira Mulungu wakuwakhululukira, mungakhale munabwezera chilango pa zochita zao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Munawayankha, Yehova Mulungu wathu: munawakhalira Mulungu wakuwakhululukira, mungakhale munabwezera chilango pa zochita zao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Inu Chauta, Mulungu wathu, munkaŵayankha, munali Mulungu woŵakhululukira, komabe wolanga ntchito zao zoipa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Inu Yehova Mulungu wathu, munawayankha iwo; Inu kwa Israeli munali Mulungu wokhululuka, ngakhale munawalanga pa zochita zawo zoyipa. Onani mutuwo |