Masalimo 99:7 - Buku Lopatulika7 Iye analankhula nao mu mtambo woti njo: Iwo anasunga mboni zake ndi malembawa anawapatsa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Iye analankhula nao mu mtambo woti njo: Iwo anasunga mboni zake ndi malembawa anawapatsa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Ankalankhula nawo mu mtambo woima kuti njo. Iwo ankasunga mapangano ndi malangizo amene Iye adaŵapatsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Iye anayankhula nawo kuchokera mʼchipilala cha mtambo; iwo anasunga malamulo ake ndi zophunzitsa zomwe anawapatsa. Onani mutuwo |