Masalimo 97:9 - Buku Lopatulika9 Pakuti Inu, Yehova, ndinu Wam'mwambamwamba padziko lonse lapansi, ndinu wokwezeka kwakukulu pamwamba pa milungu ina yonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Pakuti Inu, Yehova, ndinu Wam'mwambamwamba pa dziko lonse lapansi, ndinu wokwezeka kwakukulu pamwamba pa milungu yonse ina. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Pakuti Inu Chauta ndinu Wopambanazonse, wolamulira dziko lonse lapansi. Ndinu amphamvu kupambana milungu yonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pakuti Inu Yehova ndi Wammwambamwamba pa dziko lonse lapansi; ndinu wokwezeka kupambana milungu yonse. Onani mutuwo |