Masalimo 97:8 - Buku Lopatulika8 Ziyoni anamva nakondwera, nasekerera ana aakazi a Yuda; chifukwa cha maweruzo anu, Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ziyoni anamva nakondwera, nasekerera ana akazi a Yuda; chifukwa cha maweruzo anu, Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Anthu a ku Ziyoni akumva, ndipo akusangalala, midzi ya ku Yuda nayonso ikukondwera chifukwa cha kaweruzidwe kanu, Inu Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Ziyoni akumva ndipo akukondwera, midzi ya Yuda ikusangalala chifukwa cha maweruzo anu Yehova. Onani mutuwo |