Masalimo 97:5 - Buku Lopatulika5 Mapiri anasungunuka ngati sera pamaso pa Yehova, pamaso pa Ambuye wa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Mapiri anasungunuka ngati sera pamaso pa Yehova, pamaso pa Ambuye wa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mapiri amasungunuka ngati sera pamaso pa Chauta, ndiye wolamulira dziko lonse lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mapiri amasungunuka ngati phula pamaso pa Yehova, pamaso pa Ambuye a dziko lonse lapansi. Onani mutuwo |