Masalimo 97:4 - Buku Lopatulika4 Mphezi zake zinaunikira dziko lokhalamo anthu; dziko lapansi linaona nilinagwedezeka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Mphezi zake zinaunikira dziko lokhalamo anthu; dziko lapansi linaona nilinagwedezeka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Zing'aning'ani zake zimaŵalitsa dziko lonse lapansi, dziko lonse limapenya nkugwedezeka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Zingʼaningʼani zake zimawalitsa dziko lonse; dziko lapansi limaona ndipo limanjenjemera. Onani mutuwo |