Masalimo 93:3 - Buku Lopatulika3 Mitsinje ikweza, Yehova, mitsinje ikweza mkokomo wao; mitsinje ikweza mafunde ao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Mitsinje ikweza, Yehova, mitsinje ikweza mkokomo wao; mitsinje ikweza mafunde ao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Inu Chauta, nyanja zazikulu zakwera, zikukokoma koopsa. Mafunde ake akuchita mkokomo waukulu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Nyanja zakweza Inu Yehova, nyanja zakweza mawu ake; nyanja zakweza mafunde ake ochita mkokomo. Onani mutuwo |