Masalimo 93:4 - Buku Lopatulika4 Yehova Wam'mwamba ndiye wamphamvu, wakuposa mkokomo wa madzi ambiri, ndi mafunde olimba a nyanja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Yehova Wam'mwamba ndiye wamphamvu, wakuposa mkokomo wa madzi ambiri, ndi mafunde olimba a nyanja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Chauta amene ali pamwamba, ndi wamphamvu kupambana kulindima kwa madzi ambiri, ndi wamphamvu kuposa mafunde am'nyanja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yehova ndi wamphamvu kupambana mkokomo wa madzi ambiri, ndi wamphamvu kupambana mafunde a nyanja, Yehova mmwamba ndi wamphamvu. Onani mutuwo |