Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 87:3 - Buku Lopatulika

3 Mzinda wa Mulungu, inu, akunenerani zakukulemekezani.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Mudzi wa Mulungu, inu, akunenerani zakukulemekezani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Iwe mzinda wa Mulungu, anthu amakamba zambiri zotamanda iwe.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Za ulemerero wako zimakambidwa, Iwe mzinda wa Mulungu: Sela

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 87:3
20 Mawu Ofanana  

Pali mtsinje, ngalande zake zidzakondweretsa mzinda wa Mulungu. Malo oyera okhalamo Wam'mwambamwamba.


Tafuula, takuwa iwe, wokhala mu Ziyoni, chifukwa Woyera wa Israele wa m'kati mwako ali wamkulu.


Ndipo Mombolo adzafika ku Ziyoni, ndi kwa iwo amene atembenuka kusiya kulakwa mwa Yakobo, ati Yehova.


ndikakonzere iwo amene alira maliro mu Ziyoni, ndi kuwapatsa chovala kokometsa m'malo mwa phulusa, mafuta akukondwa m'malo mwa maliro, chovala cha matamando m'malo mwa mzimu wopsinjika; kuti iwo atchedwe mitengo ya chilungamo yakuioka Yehova, kuti Iye alemekezedwe.


Atero Ambuye Yehova, Popeza mdani ananena za inu, Ha! Ingakhale misanje yakale ili yathu, cholowa chathu;


Atero Yehova Mulungu, Uwu ndi Yerusalemu ndinauika pakati pa amitundu, ndi pozungulira pake pali maiko.


Ndipo ndinapenya, taonani, Mwanawankhosayo alikuimirira paphiri la Ziyoni, ndipo pamodzi ndi Iye zikwi zana mphambu makumi anai kudza anai, akukhala nalo dzina lake ndi dzina la Atate wake lolembedwa pamphumi pao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa