Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 87:2 - Buku Lopatulika

2 Yehova akonda zipata za Ziyoni koposa zokhalamo zonse za Yakobo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Yehova akonda zipata za Ziyoni koposa zokhalamo zonse za Yakobo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Chauta amakonda mzinda wa Ziyoni amaukonda kupambana kwina kulikonse kumene zidzukulu za Yakobe zimakhala.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Yehova amakonda zipata za Ziyoni kupambana malo onse okhalamo a Yakobo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 87:2
7 Mawu Ofanana  

Koma ndinasankha Yerusalemu, kuti dzina langa likhale komweko; ndinasankhanso Davide akhale mfumu ya anthu anga Israele.


Ndipo adzayankhanji amithenga a amitundu? Kuti Yehova wakhazikitsa Ziyoni, ndipo m'menemo anthu ake ovutidwa adzaona pobisalira.


Ndipo padzakhala masiku otsiriza, kuti phiri la nyumba ya Yehova lidzakhazikika pansonga ya mapiri, ndipo lidzakwezedwa pamwamba pa zitunda; mitundu yonse idzasonkhana kumeneko.


Ndipo kudzachitika kuti aliyense adzaitana pa dzina la Yehova adzapulumutsidwa; pakuti m'phiri la Ziyoni ndi mu Yerusalemu mudzakhala chipulumutso, monga Yehova anatero, ndi mwa otsala amene Yehova adzawaitana.


Koma kumalo amene Yehova Mulungu wanu adzasankha mwa mafuko anu onse kuikapo dzina lake, ndiko ku chokhalamo chake, muzifunako, ndi kufikako;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa