Masalimo 85:3 - Buku Lopatulika3 Munabweza kuzaza kwanu konse; munabwerera kumkwiyo wanu wotentha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Munabweza kuzaza kwanu konse; munabwerera kumkwiyo wanu wotentha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Mudaleka ndithu ukali wanu woopsa, mudaletsa mkwiyo wanu woyaka moto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Munayika pambali ukali wanu wonse ndi kutembenuka kuchoka ku mkwiyo wanu woopsa. Onani mutuwo |