Masalimo 85:2 - Buku Lopatulika2 Munachotsa mphulupulu ya anthu anu, munafotsera zolakwa zao zonse. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Munachotsa mphulupulu ya anthu anu, munafotsera zolakwa zao zonse. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Mudakhululukira machimo a anthu anu, mudafafaniza zolakwa zao zonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Munakhululukira mphulupulu za anthu anu ndi kuphimba machimo awo onse. Sela Onani mutuwo |