Masalimo 85:1 - Buku Lopatulika1 Munachita zovomereza dziko lanu, Yehova; munabweza ukapolo wa Yakobo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Munachita zovomereza dziko lanu, Yehova; munabweza ukapolo wa Yakobo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Inu Chauta, mudakomera mtima dziko lanu, mudaŵakhazikanso pabwino a m'banja la Yakobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova munakomera mtima dziko lanu; munabwezeretsa ulemerero wa Yakobo. Onani mutuwo |