Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Masalimo 84:12 - Buku Lopatulika

12 Yehova wa makamu, wodala munthu wakukhulupirira Inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Yehova wa makamu, wodala munthu wakukhulupirira Inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Inu Chauta Wamphamvuzonse, ngwodala munthu woika chikhulupiriro chake pa Inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Inu Yehova Wamphamvuzonse, wodala ndi munthu amene amakhulupirira Inu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 84:12
10 Mawu Ofanana  

Chitirani chokoma, Yehova, iwo okhala okoma; iwo okhala oongoka mumtima mwao.


Mpsompsoneni Mwanayo, kuti angakwiye, ndipo mungatayike m'njira ukayaka pang'ono pokha mkwiyo wake. Odala onse akumkhulupirira Iye.


Ndifuula kwa Yehova ndi mau anga, ndipo andiyankha m'phiri lake loyera.


Talawani, ndipo onani kuti Yehova ndiye wabwino; wodala munthuyo wakukhulupirira Iye.


Khulupirirani pa Iye nyengo zonse, anthu inu, tsanulirani mitima yanu pamaso pake. Mulungu ndiye pothawirapo ife.


Chifukwa chake Yehova adzadikira, kuti akukomereni mtima, ndipo chifukwa chake Iye adzakuzidwa, kuti akuchitireni inu chifundo; pakuti Yehova ndiye Mulungu wa chiweruziro; odala ali onse amene amdikira Iye.


Ndani ali mwa inu amene amaopa Yehova, amene amamvera mau a mtumiki wake? Iye amene ayenda mumdima, ndipo alibe kuunika, akhulupirire dzina la Yehova, ndi kutsamira Mulungu wake.


Dzuwa silidzakhalanso kuunika kwako usana, ngakhale mwezi sudzakuunikiranso kuti kuyere; koma Yehova adzakhala kwa iwe kuunika kosatha, ndi Mulungu wako adzakhala ulemerero wako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa