Masalimo 83:4 - Buku Lopatulika4 Amati, Tiyeni tiwaononge asakhalenso mtundu wa anthu; ndipo dzina la Israele lisakumbukikenso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Amati, Tiyeni tiwaononge asakhalenso mtundu wa anthu; ndipo dzina la Israele lisakumbukikenso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Iwo amati, “Tiyeni tifafanize mtundu wao wonse. Dzina la Israele lisakumbukikenso.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Iwo akunena kuti, “Bwerani” akutero, “Tiyeni tiwononge mtundu wonsewu kuti dzina la Israeli lisakumbukikenso.” Onani mutuwo |