Masalimo 83:3 - Buku Lopatulika3 Apangana mochenjerera pa anthu anu, nakhalira upo pa obisika anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Apangana mochenjerera pa anthu anu, nakhalira upo pa obisika anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Akuchitira anthu anu upo wonyenga. Akuŵapangira zoipa anthu anu amene mumaŵateteza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Mochenjera iwo akukambirana za chiwembu kutsutsana ndi anthu anu; Iwo akukonzekera kutsutsana ndi omwe mumawakonda. Onani mutuwo |