Masalimo 83:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti taonani, adani anu apokosera, ndipo okwiyira Inu aweramutsa mutu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti taonani, adani anu aphokosera, ndipo okwiyira Inu aweramutsa mutu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Onani, adani anu akuchita chiwawa. Amene adana nanu akukuukirani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Onani adani anu akuchita chiwawa, amene amadana nanu autsa mitu yawo. Onani mutuwo |