Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 83:1 - Buku Lopatulika

1 Mulungu musakhale chete; musakhale duu, osanena kanthu, Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Mulungu musakhale chete; musakhale duu, osanena kanthu, Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Inu Mulungu, musakhalenso chete. Musangoti phee, musangoti duu, Inu Mulungu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Inu Mulungu musakhale chete; musangoti phee, Mulungu musangoti duu.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 83:1
7 Mawu Ofanana  

Kwa Inu, Yehova, ndidzafuulira; thanthwe langa, musandikhalire ngati wosamva; pakuti ngati munditontholera ine, ndidzafanana nao iwo akutsikira kumanda.


Yehova, mudazipenya; musakhale chete, Ambuye, musakhale kutali ndi ine.


Galamukani, mugoneranji, Ambuye? Ukani, musatitaye chitayire.


Mulungu wa milungu, Yehova, wanena, aitana dziko lapansi kuyambira kutuluka kwa dzuwa kufikira kulowa kwake.


Adzafika Mulungu wathu, ndipo sadzakhala chete. Moto udzanyeka pankhope pake, ndipo pozungulira pake padzasokosera kwakukulu.


Ndakhala nthawi yambiri wosalankhula ndakhala chete kudzithungata ndekha; tsopano ndidzafuula ngati mkazi wobala; ndidzapuma modukizadukiza ndi wefuwefu pamodzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa