Masalimo 83:17 - Buku Lopatulika17 Achite manyazi, naopsedwe kosatha; ndipo asokonezeke, naonongeke. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Achite manyazi, naopsedwe kosatha; ndipo asokonezeke, naonongeke. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Achitedi manyazi ndi mantha mpaka muyaya, ndipo afe imfa yonyozeka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Achite manyazi ndi mantha nthawi zonse; awonongeke mwa manyazi. Onani mutuwo |