Masalimo 83:16 - Buku Lopatulika16 Achititseni manyazi pankhope pao; kuti afune dzina lanu, Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Achititseni manyazi pankhope pao; kuti afune dzina lanu, Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Inu Chauta, muŵachititse manyazi, kuti azifunafuna dzina lanu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Muphimbe nkhope zawo ndi manyazi kuti adzafunefune dzina lanu Yehova. Onani mutuwo |