Masalimo 8:3 - Buku Lopatulika3 Pakuona ine thambo la kumwamba lanu, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene munazikhazika, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Pakuona ine thambo la kumwamba lanu, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene munazikhazika, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndikamayang'ana ku thambo lanu limene mudapanga ndi manja anu, ndikamaona mwezi ndi nyenyezi zimene mudazikhazika kumeneko, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pamene ndilingalira za mayiko anu akumwamba, ntchito ya zala zanu, mwezi ndi nyenyezi, zimene mwaziyika pa malo ake, Onani mutuwo |