Masalimo 75:3 - Buku Lopatulika3 Lasungunuka dziko lapansi, ndi onse okhalamo; ndinachirika mizati yake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Lasungunuka dziko lapansi, ndi onse okhalamo; ndinachirika mizati yake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Pamene dziko lapansi likugwedezeka pamodzi ndi zonse zokhalamo, ndine amene ndimachirikiza mizati yake.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Pamene dziko lapansi ndi anthu ake onse anjenjemera, ndine amene ndimagwiriziza mizati yake molimba. Sela Onani mutuwo |